Sermon synopsis: Kuuka kwa kufa kwa Ambuye Yesu ndi chikhulupiliro chakuti Yesu atafa adakhalanso ndi moyo patsiku loyamba lasabata patatha masiku atatu iye ataikidwa mmanda. Mmawu achikhulupiriro chathu muli mawu akuti, Ndipo patsiku lachitatu adauka kwa akufa monga mwa malemba.