TCHIMO NDI CHISOMO (Sin and Grace)
SERMON TOPIC: TCHIMO NDI CHISOMO (Sin and Grace)
Speaker: Ken Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 28 November 2017
Topic Groups:
Sermon synopsis: Sitiyenera kufuna funa kumene tingakapeze uchimo, uchimo uli kale
mkati mwathu.
“Zikadakhala zosavuta uchimo ukudakhala mwa anthu owerengeka
chifukwa oipawo akadapatulidwa padera ndi kuwawononga. Koma
uchimo ulimwa ife tonse ndipo palibe amene angafune kuti awononge
mtima wake.' -Adatero bambo Aleksandr Solzhenitsyn
IP:Country:City:Region:
|