What is wrong with Christians (CHICHEWA)

SERMON TOPIC: What is wrong with Christians (CHICHEWA)

Speaker: Ken Paynter

Language: CHICHEWA

Date: 1 September 2015

Topic Groups:

Sermon synopsis: KUTEMBENUKA KOSAKHALA KWENIKWENI
Kutembenuka mtima ndiko kubadwanso mwatsopano . Panyengo yakutembenuka mtima okhulupirira amasandulika mtima mwa Mzimu Oyera ndipo amayamba ulemdo osiyana ndi machimo kuyamba moyo watsopano osiyana ndi moyo woyamba umene iye amayendamo. Munthu otembenuka mtimayu amayamba kulambirta Mulungu mwa Mzimu Oyera. Kutembenuka kwa boza sikukhala kwemikweni ngakhale kumaoneka ngati kuli kuchokera kwa Mzimu Oyera. Si anthu onse amene amanena kuti ali otembenuka mtima kuti amakhala atalandira kutembenuka mtima kwenikweni.

Mufanizo la nansongole mbuku la Mateyu 13:24–30 Satana amagwira ntchito yosokoneza mpingo posakaniza mu mpingo iwo amene ali ake ndi iwo amene ali a Mulungu kuti anthe azilephera kudziwa iwo amene ali a Ambuye ndi iwo amene ali a Satana.
- Download notes (912 KB, 1600 downloads)

- All sermons by Ken Paynter

- All sermons in CHICHEWA




IP:Country:City:Region: