KUKHALA NDI MOYO OYAMIKIRA KUSIYANA NDI KUZIKUNDIKIRA
SERMON TOPIC: KUKHALA NDI MOYO OYAMIKIRA KUSIYANA NDI KUZIKUNDIKIRA
Speaker: Ken Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 23 June 2015
Topic Groups:
Sermon synopsis: KUZIKUNDIKIRA: Ndi moyo ofuna kukhala ndi zinthu zonse za pamwamba kapena kufuna ulemu wina wapadera. 2 Timoteo 3:1-5 Masiku otsiriza anthu adzakhala osayamika. Chikhalidwe china cha anthu osapembedza Mulungu chikuwonetseredwa mbuku la Aroma 1:21 Sitikuyenera kungokhutira chabe pazinthu zimene Ambuye alikutichitira komanso tikuyenera kuwonetsera poyamikira.
IP:Country:City:Region:
|