Sermon No: 2623-The value of a soul - Part 3 (CHICHEWA)SERMON TOPIC: The value of a soul - Part 3 (CHICHEWA)Speaker: Gavin PaynterLanguage: CHICHEWA Date: 30 March 2015Topic Groups: Sermon synopsis: Q: Kodi moyo wanu ndi wa mtengo wapatali bwanji kwa inu?
A: Moyo wanu ndiye chuma choposa chuma chirichonse chimene mungathe kukhala nacho.
Moyo uposa thupi:
Mateyu 10:28 Ndipo musamaopa amene akupha thupi, koma moyo sangathe kuupha. Moyo uli wa mtengo wake wapatali kuposa chuma chonse cha dziko lapansi:
Mateyu 16:26 Pakuti munthu adzapindulanji akalandira dziko lonse lapansi nataya moyo wake? Kapena munthu adzaperekenji chosintha ndi moyo wake? IP:Country:City:Region: |