The book of life
SERMON TOPIC: The book of life
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 15 February 2015
Topic Groups:
Sermon synopsis: Mneneri wa Mulungu Mose adanena kuti Mulungu ali Ndi Buku la kulembamo: Eksodo 32:32 “… Ngati mukana mundifafanizetu, kundichotsatu mbuku lanu limene munalembera.” Mtumwi Yohane ali kunenana kuti Buku lotchedwa “Buku la moyo”Ndilo la Mwana wa nkhosa( Yesu) Chibvumbulutso 13:8 …Mbuku lamoyo la mwana wa nkhosa wophedwa kuyambira makhazikidwe adziko lapansi.
IP:Country:City:Region:
|