Calvinism - Part 6a -The atonement - CHICHEWA
SERMON TOPIC: Calvinism - Part 6a -The atonement - CHICHEWA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 26 May 2017
Topic Groups: CALVINISM, ARMINIANISM
Sermon synopsis: TANTHAUZO ; Mau akuti atonement ndi mau amene alibe mau ambiri owatanthawuzira muchingerezi. Mau akuti atonement adalumikidzidwa ndi ndi William Tyndale ndipo muchingerezi amatanthawuza kuti, at---one---ment i.e. kutanthauza kukhalanso mu ummodzi kapena kuti kuyanjanitsidwanso ndi munthu wina.
IP:Country:City:Region:
|