Last words of Jesus - The great commission - CHICHEWA.

SERMON TOPIC: Last words of Jesus - The great commission - CHICHEWA

Speaker: Gavin Paynter

Language: CHICHEWA

Date: 15 August 2014

Topic Groups:

Sermon synopsis: Pamene wina ali pafupi kusiyana nafe munjira ya imfa kapenanso ulendo wautali, mau omwe amawalankhula amakhala ofunika kwambiri mwinanso kuposera ena onse omwe adawalankhula kale asanasiyane nanu.
Munthawi yakusiyanayi sipakhalanso kutaya nthawi ndikufotokoza zina ndi zina zopanda pake popeza nthawiyi imakhala yochepa. Choncho zomwe zimalankhulidwa ngati mau otsiliza zimakhala zamphamvu, zaphindu ndi zofunika kuzitsatira kwa otsala. Izi tikuziona munkhani ya Yesu mu mau ake otsiliza.
Ena mwa mau otsiliza omwe Yesu adawalankhula atauka kwa kufa komanso asanakwere kunka kumwamba ndi mau omwe amatchedwa kuti Utumwi, “Great Commission” pachingerezi.
- Download notes (4.85 MB, 1200 downloads)

- All sermons by Gavin Paynter

- All sermons in CHICHEWA




IP:Country:City:Region: