Last words of Jesus - The great commission - CHICHEWA
SERMON TOPIC: Last words of Jesus - The great commission - CHICHEWA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 15 August 2014
Topic Groups:
Sermon synopsis: Pamene wina ali pafupi kusiyana nafe munjira ya imfa kapenanso ulendo wautali, mau omwe amawalankhula amakhala ofunika kwambiri mwinanso kuposera ena onse omwe adawalankhula kale asanasiyane nanu. Munthawi yakusiyanayi sipakhalanso kutaya nthawi ndikufotokoza zina ndi zina zopanda pake popeza nthawiyi imakhala yochepa. Choncho zomwe zimalankhulidwa ngati mau otsiliza zimakhala zamphamvu, zaphindu ndi zofunika kuzitsatira kwa otsala. Izi tikuziona munkhani ya Yesu mu mau ake otsiliza. Ena mwa mau otsiliza omwe Yesu adawalankhula atauka kwa kufa komanso asanakwere kunka kumwamba ndi mau omwe amatchedwa kuti Utumwi, “Great Commission” pachingerezi.
IP:Country:City:Region:
|