Sermon synopsis: Yakobo 3:9-10 imayamika Ambuye ndi Atate nalo; naloso timatemberera anthu okhala monga mwamafanizidwe a Mulungu. Mochokera mkamwa momwqemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga izi siziyenera kutero.
Yakobo 1:26 Ngati wina adziyesera ali wopembedza Mulungu, ndiye wosamanga lilime lake, koma adzinyenga mtima wake, kupembedza kwake kwa munthuyo nkonama.
1 Petro 3:10 Pakuti iye wofuna kukonda moyo ndikuona masiku abwino, aletse lilime lake lisanene choipa ndi milomo yake isalankhule chinyengo.