Chikondi (Love)
SERMON TOPIC: Chikondi (Love)
Speaker: Ken Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 26 May 2014
Topic Groups:
Sermon synopsis: Imodzi mwa mitu yamphamvu ya ulakatuli mu Baibulo, 1 Akolinto 13, mtumwiPaulo akufotokoza za mtundu wachikondichomwe akhristuayenera kukhala nacho: “Chikondi chikhala chilezere,chiri chokoma mtima;chikondi sichidukidwa; chikondi sichidziwakudzitamanda, sichidzikuza, , sichichita zosayenera,sichitsata zamwini yekha, sichipsa mtima,sichilingalira zoipa; sichikondwera ndichinyengo, koma hikondwera ndichoonadi; chikwilira zinthu zonse, chikhulupilira zinthu zonse,chiyembekeza zinthu zonse, chipilira zinthu zonse. Chikondi sichilephera.'
IP:Country:City:Region:
|