Contentment - CHICHEWA
SERMON TOPIC: Contentment - CHICHEWA
Speaker: Ken Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 30 April 2014
Topic Groups:
Sermon synopsis: Ahebri 13:5 “Sindidzakusiyani konse, kungakhale kukutaya, sindidzakutaya ndithu.”
Ahebri 13:5 Ndi ndime yodziwika, koma ndi gawo limodzi lavesi, sivesi la thunthu loyima palokha. Ndime yonse ya vesili limati;
Mtima wanu ukhale osakonda chuma, zimene muli nazo zikukwanireni;pakuti Iye anati, Sindidzakusiya konse, kungakhale kukutaya, sindidzakutaya ndithu.
IP:Country:City:Region:
|