The cares of this life - CHICHEWA

SERMON TOPIC: The cares of this life - CHICHEWA

Speaker: Ken Paynter

Language: CHICHEWA

Date: 5 April 2014

Topic Groups:

Sermon synopsis: KODI MWAPSINJIKA NDINKHAWA ZA MOYO UNO?
MULUNGU AKUTI MUMUTULIRE IYE.

1 PETRO 5:6-7 Potero dzichepetseni pansi pa dzanja la mphamvu la Mulungu, kuti pantawi yache akukwezeni;ndi kutaya pa iye nkhawa yanu yonse, pakuti iye asamalira inu.

MAU A MULUNGU AMATIUZA KUTI NJIRA YABWINO YOMWE TINGAONETSERE KUDZICHEPETSA, NDIYO POMWE TISANKHA KUTULA NKHAWA ZATHU PA MULUNGU.

“TAYANI NKHAWA ZANU ZONSE” PA IYE – TKUZINDIKIRA KOMANSO KUVOMEREZA KUTI PA WEKHA SUNGAKWANITSE KUPEZA NJIRA PA WEKHA YOTHANIRANA NDI NKHAWA ZAKO.
- Download notes (586 KB, 1264 downloads)

- All sermons by Ken Paynter

- All sermons in CHICHEWA




IP:Country:City:Region: