Sermon synopsis: Chiphunzitso cha paphiri ndi m’ndandanda wa ziphunzitso zomwe Yesu adaphunzitsa pa phiri, kuchokera pa Mateyu 5:3-12.
Mau akuti Chiphunzitso chapaphiri, mukumasulira kwina kwa chingerezi amatchedwa kuti ‘beatitude’ ndipo amapangidwa kuchokera ku m’fotokozi wa mau achi ‘Latin’ otchedwa ‘beatus’ omwe tanthauzo lake mu chichewa ndi kukondwa, mwai kapenanso kuti chimwemwe chopitilira muyeso chauzimu.