Do Muslims worship the same God as Christians - Part 1 - CHICHEWA
SERMON TOPIC: Do Muslims worship the same God as Christians - Part 1 - CHICHEWA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 7 March 2014
Topic Groups:
Sermon synopsis: Pongoyang’ana ndi maso, Chisilamu chiri ndi mayambidwe ofanana ndi zipembedzo za Judaism komanso Chikhristu
Asilamu amakhulupilira Mulungu mmodzi , mlengi wa zonse.
Chisilamu chidachokera mufuko la Abrahamu ndipo chimalemekeza Nowa, Mose, Abrahamu ndi Solomoni komanso Yesu monga aneneri.
Asilamu amabvomereza Chipangano Chakale ndi chatsopano komanso amayang’anira kubweranso kwachiwiri kwa Yesu Khristu kudzaweruza dziko lapansi. Iwo amamutchula Yesu kuti (Isa)
Koma mchiphunzitso chawo chiri chotsutsana ndi Baibulo kuyang’anira mmene Korani imaphunzitsira mmene msilamu angawonere zinthu zokhuza Munthu wa Mkazi, maka maka amene si asilamu, komanso iwo amene ali Ayuda.
IP:Country:City:Region:
|