UTUMIKI WA MZIMU WOYERA
SERMON TOPIC: UTUMIKI WA MZIMU WOYERA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 1 March 2014
Topic Groups:
Sermon synopsis: Q: Kodi cholinga cha ubatizo wa Mzimu Woyera ndi chiyani? Kodi ndi chakuti anthu alankhule ndi malilime ndi kuchita zodabwitsa. Kapena adzigwetse ndimavina vina?
A: AYI – Ambuye Yesu adapereka chifukwa choyambirira kwa ophunzira ake pamene adawawuza kuti adikirire ku Yerusalemu lonjezano la Mzimu Woyera.
Machitidwe 1:8 “Komatu mudzalandira mphamvu Mzimu Woyera atadza pa inu, Ndipo mudzakhala mboni zanga M’yerusalemu ndi Myudeya,ndi Msamariya, ndikufikira malekezero ake adziko lapansi.”
Cholinga choyambirira chakudzadzidwa ndi Mzimu Woyera ndi chakuti tilalikire uthenga wabwino kudziko lonse lapansi, kudzera njira ya usodzi komanso utumwi.
IP:Country:City:Region:
|