Sermon synopsis: Munjira imeneyi, Abrahamu amafaniziridwa ndi a Khristu ammene ali monga alendo padziko lino lapansi, amene mwa chikhulupiliro ali kuyang’anira dziko labwino- dziko lakumwamba.
Ahebri 11:13-14 Iwo onse adamwalira mchikhulupiliro, osalandira malonjezano, komatu adawona kutali,nabvomereza kuti ali alendo ndi ogonera padziko. Pakuti iwo akunena zotere awonetserapo kuti alikufuna kuti dziko likhale lawo.