INU NDINU MCHERE
SERMON TOPIC: INU NDINU MCHERE
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 19 November 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: MATEYU 5:13-16 “Inu ndinu m’chere wadziko lapansi; koma mcherewo ngati ukasukuluka, adzaukoleretsa ndi chiyani? Pamenepo sungakwanirenso kanthu konse, koma kuti ukaponyedwe kunja nupondedwe ndi anthu. Inu ndinu kuunika kwa dziko lapansi. Mudzi okhazikika pamwamba pa phiri sungathe kubisika. Kapena sayatsa nyali ndi kuivundikira m’mbiya koma aiika iyo pachoikapo pake; ndipo iunikira onse ali m’nyumbamo. Chomwecho muwalitse inu kuunika kwanu pamaso pa anthu, kuti pakuona ntchito zanu zabwino, alemekeze Atate anu a kumwamba.”
IP:Country:City:Region:
|