CHIPHUNZITSO CHA CHIPULUMUTSO - Gawo 2
SERMON TOPIC: CHIPHUNZITSO CHA CHIPULUMUTSO - Gawo 2
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 16 November 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: Chikhristu chimaphunzitsa kuti Yesu simunthu wamba, mneneri, koma, Mpulumutsi wadziko lonse ,”dzina lokhalo pansi pa thambo lopatsidwa kwa anthu lomwe tipulumutsidwa nalo.” (Machitidwe 4:12) Aefeso 2:13-18 Koma tsopano mwa Yesu Khristu inu amene munali kutali kale, anakusendezani mukhale pafupi m’mwazi wa Khristu. Pakuti Iye ndiye mtendere wathu, amene anachita kuti onse awiri akhale m’modzi, nagumula khoma lakudulitsa pakati,… ndikuti akayanjanitse awiriwa m’thupi limodzi mwamtandawo atapha nawo udaniwo; kuti mwa Iye ife tonse awiri tili nawo malowedwe athu kwa Atate, mwa Mzimu mmodzi.
IP:Country:City:Region:
|