Chipambano kapena Kukhulupirika (Success or faithfulness)
SERMON TOPIC: Chipambano kapena Kukhulupirika (Success or faithfulness)
Speaker: Ken Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 10 November 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: Mulungu sakutifunsa kuti tikapambane pachiri chonse chimene tirikuchita, koma kuti tikhale okhulupilika. Adatero mayi wina wodziwika ndi ntchito zachifundo wotchedwa. (Mayi Teresa) Nthawi zonse pamene ndiwonera matchanero ambiri amawayilesi akanema, ndimakhala odabwa kuona alaliki ambiri amene amalalikira uthenga owaonetsera anthu kuti kukhala ndi chuma komanso moyo wathanzi ndi chizindikiro chokhala mkhristu wabwino Izi ndizimene athu ambiri amazikonda komanso amazikhulupirira komabe pamapeto ake amakhumudwitsidwa komanso kuchepetsedwa pa chikhulupiriro chimene alinacho. Cholinga chathu choyambirira chisakhale kupambana koma kukhala okhulupirika munyengo iliyonse.
IP:Country:City:Region:
|