Temptation
SERMON TOPIC: Temptation
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 10 October 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: Yesero ndi zochitika zimene zimaoneka zokopa kwa munthu.Makopedwewa amabweretsa kumva kutsutsika chifukwa amatsogolera munthu kukachita chinthu chotsutsana ndi chimene iye amafuna. Mayesero amatanthauziranso kuchita chinthu choipa mowumirizidwa kapena mwamantha.Tingatanthauzilenso kuti Yesero ndi mchitidwe okopa kapena kupangilidwa ndi wena kuchita chinthu cholakwika poganizira kuti pamapeto ake tipeza chisangalaro.Komanso yesero likhoza kukhala chinthu chiri chonse chimene chiri ndi makopedwe. Kutanthauzira kwinanso kukhoza kukhala kwa kuti, yesero ndi chilakolako chofuna kuchita kapena kukhala ndi chinthu chimene sukuyenera kukhala nacho kapena kuchichita.
IP:Country:City:Region:
|