Sermon No: 1320-NkhawaSERMON TOPIC: Nkhawa, Kupsinjika mumtima ndi MadandauloSpeaker: Gavin PaynterLanguage: CHICHEWA Date: 10 October 2013Topic Groups: Sermon synopsis: Mlakatuli komanso mtumiki wachikhristu ku Scotland, George MacDonald adati; “Sizosamalira moyo zalero, zomwe zimamusautsa munthu, koma zamawa.”
“Nkhawa siyikuba chisoni cha mawa, koma imangoyamwa chimwemwe cha lero.” (Leo Buscaglia)
“Nkhawa kawirikawiri imapereka chithunzithunzi chachikulu kwa kanthu kakang’onong’ono.” (Swedish Proverb)
“Sintchito yomwe imapha, koma nkhawa.” (African Proverb) IP:Country:City:Region: |