CHOLINGA CHA MASAUTSO

SERMON TOPIC: CHOLINGA CHA MASAUTSO

Speaker: Gavin Paynter

Language: CHICHEWA

Date: 21 September 2013

Topic Groups:

Sermon synopsis: Baibulo limatipatsa chidwi chochuruka pazimene lima nena za choonadi cheni cheni cha masautso. Ilo sirinena za masautso monga chionongeko monga mnene zipembezo zina zonama zimakhulupirira kapena kuchitira mopyolera muyeso. Limodzi mawa mabuku akulu amBaibulo, buku la Yobu linaperekedwa kukayankha funsoli. Mabuku a Yeremiya ndi Habakuku ali ndi zambiri zonena zokhuza nkhani imeneyi. Ndime zochuruka za buku la masalimo, ndimapemphero amchipangano chakale, ndikulira kochokera mchikaiko, kukhumudwitsidwa komanso kumva ululu.

Zolemba zambiri za buku la Petro woyamba komanso buku la Ahebri ndi zokhuza masautso a aKhristu. Makalata aPaulo ochuruka analemba ali mundende.
Kodi masautso mkukhala cholinga cha Mulungu? ZOONA!
Petro analemba kuti, koteronso iwo akumva zowawa monga mwachifuniro cha Mulungu aike moyo wawo ndikuchita zokoma mmanja awolenga wokhulupirika...” (1 Petro 4:19)
Pakuti kumva zowawa chifukwa chakuchita zabwino, ndikumva zowawa chifukwa chakuchitra zoipa, mkwabwino kumva zowawa chifukwa chakuchita zabwino, ngati chiterotu chifuniro cha Mulungu. (1 Petro 3:17)

- Download notes (1.04 MB, 1743 downloads)

- Download audio (12.45 MB, 1684 downloads)
- All sermons by Gavin Paynter

- All sermons in CHICHEWA




IP:Country:City:Region: