Sermon synopsis: Ogulitsa nsapato wina oyambirira wotcedwa D.L. Moody adati “Ngati dziko lapansi lingafikiridwe, Ndiri kutsikimizira kuti,
izi ziyenera kuchitika ndi abambo kapena amayi aluso lawo lochuruka. Koma pali anthu ochepa padziko lapansi amene ali ndi luso lochurukalo.
Hudson Taylor adati, “Mulungu Sali kuyang’ana anthu achikhulupiro chachikuru, koma anthu amene ali okonzeka kumutsatira”
ndipo 'Mulungu amagwiritsa anthu ofoka amene ali kutsamira paiye kwathunthu.”