Setting the captives free - CHICHEWA
SERMON TOPIC: Setting the captives free - CHICHEWA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 22 August 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: KAMASULIRIDWE KA MAWU A UKAPOLO KOLINGANA NDI BAIBULO :Munthu amakhala kapolo wa chilichonse chomwe chimamulamulira:
2 Pet 2:19 ndikuwalonjeza iwo ufulu, pokhala iwo okha ali akapolo a chivundi;—pakuti munthu ndi kapolo wa chilichonse
chomwe chimamulamulira.
Arom 6:16 Kodi simudziwa kuti kwa iye amene mudzipereka eni nokha kukhala akapolo ake a yemweyo mulikumvera iye;
kapena auchimo kulinga kuimfa, kapena aumvero kulinga kuchilungamo?
Tchimo ndi chivundi zimapatsa ukapolo:
Miyambo 5:22 Zoipa zake zake zidzagwira; Adzamangidwa ndi zingwe za uchimo wake.
Agalatiya 3:22 Komatu lembo linatsekereza zonse pansi pa uchimo kuti lonjezano lakwachikhulupiliro cha Yesu Khristu
likapatsidwe kwa okhulupilirawo.
IP:Country:City:Region:
|