Generational curses (CHICHEWA)

SERMON TOPIC: Generational curses (CHICHEWA)

Speaker: Ken Paynter

Language: CHICHEWA

Date: 6 July 2013

Topic Groups:

Sermon synopsis: Chinthu ichi chotchedwa themberero chiri ndi maonekedwe amakopedwe kwa anthu ambiri. Nthawi zambiri anthu amene atembenuka mtima magulu aanthu akuda khungu amene anali kupembeza mizimu ya makolo awo amene anafa, amalozedwa chala kuti iwo amabweretsa ziwanda muchipembedzo cha Chikhristu. Koma sitirikuchita bwino pamene tiri kubweretsa zinthu zachilendo komanso mantha muchipembedzo chathu cha Chikhristu, pakuchititsa kuti anthu ena akakaiyike kuti mwazi wa Yesu umene unaperekedwa kukhala nsembe yotitsukira machimo athu, kuti singathenso kutimasura kuzinthu za kale lathu. Ichi chotchedwa “chapadera kapena chinachake” kuti munthu akadutsenso mumadongosolo ene kapena kukawonana ndi munthu wina amene ali ndi kuthekera kwa maphunziro ena; kuti akatimasure kumzere wamatemberero ochokera kumtundu wathu kapena kuti makolo athu chiri kuphwanyidwa ndi mau aMulungu opezeka pa 1 Akorinto 5:17 mau Amulungu akuti:
“Chifukwa chake ngati munthu aliyense ali mwa Khristu ali wolengwedwa mwatsopano; zinthu zakale zapita taonani zakhala zatsopano”

- Download notes (84 KB, 1664 downloads)

- Download audio (9.92 MB, 1504 downloads)
- All sermons by Ken Paynter

- All sermons in CHICHEWAPDF sermon

IP:Country:City:Region: