Sermon synopsis: Anthu ambiri amapanga madongosolo ambiri m’moyo komasadziwa tsiku la imfa yawo.
Yakobo 4:13-14
Nanga tsono, inu akunena, lero kapena mmawa tidzapita kulowa kumudzi wakuti wakuti, ndipotidzagonerako ndi kutsatsa malonda, ndikupindula nawo; inu amene simudziwa chimene chidzagwa mmawa.