MAZIKO OKHAZIKIKA 6 - CHIWERUZO CHA MUYAYA
SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 6 - CHIWERUZO CHA MUYAYA
Speaker: David Makiyi
Language: CHICHEWA
Date: 5 June 2013
Topic Groups: 1ST PRINCIPLES
Sermon synopsis: Aroma 2:5-11 Koma kolingana ndikuuma kwako,ndimtima wako osalapa, ulikudziunjikira wekha mkwiyo padzuwa la mkwiyo ndi la kubvumbulutsa kuweruza, adzabwezera munthu aliyense kolingana ndi ntchito zache; kwa iwo amene anafunafuna ulemerero ndi ulemu ndichisaonongeko, mwakupilira pantchito zabwino adzabwezera moyo osatha; koma kwa iwo andeu, ndi osamvera choonadi,koma amvera chosalungama, adzabwezera mkwiyo ndi kuzaza,nsautso ndikuwawa mtima, kwa moyo wa munthu aliyense wakuchita zoipa kuyambira Myuda,komanso Mhelene; pakuti Mulungu alibe tsankhu.
IP:Country:City:Region:
|