MAZIKO OKHAZIKIKA 5 - ZA KUUKA KWA AKUFA
SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 5 - ZA KUUKA KWA AKUFA
Speaker: David Makiyi
Language: CHICHEWA
Date: 5 June 2013
Topic Groups: 1ST PRINCIPLES
Sermon synopsis: Yohane 5:21,24
'Pakuti monga Atate aukitsa akufa, nawapatsa moyo,momwemonso mwana apatsa moyo iwo amene Iye afuna. 24 'Indetu indetu ndinena kwa inu,kuti iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira Iye amene Anandituma Ine,alinawo moyo wosatha ndipo salowa mkuweruza koma wachokera ku imfa,nalowa mmoyo.”
IP:Country:City:Region:
|