MAZIKO OKHAZIKIKA 3 - CHIPHUNZITSO CHA UBATIZO
SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 3 - CHIPHUNZITSO CHA UBATIZO
Speaker: David Makiyi
Language: CHICHEWA
Date: 7 June 2013
Topic Groups: 1ST PRINCIPLES
Sermon synopsis: Nthawi zambiri timakhala ndi chidziwitso cha ma ubatizo atatu akulu amuBaibulo. Koma tiyenera kudziwa kuti Baibulo limanenanso za ubatizo wa chinayi sikuyenera kukhala osaudziwa. Mu chiphunzitso chathu cha ‘Ubatizo’, tifotokozera magawo anai aubatizo amene akupezeka mmawu a Mulungu:
IP:Country:City:Region:
|