MAZIKO OKHAZIKIKA 4 - KUSANJIKA MANJA
SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 4 - KUSANJIKA MANJA
Speaker: David Makiyi
Language: CHICHEWA
Date: 6 June 2013
Topic Groups: 1ST PRINCIPLES
Sermon synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi)
Mawu otsogolera
Mariko 16:17-18 'Ndipo zizindikilo izi zidzawatsata iwo akukhulupilira: mdzina langa adzatulutsa ziwanda; adzalankhula ndi malankhulidwe atsopano; adzatola njoka ndipo ngakhale akamwa kanthu kakufa nako sikadzawapweteka; adzaika manja awo pa odwala ndipo adzachira.'
2 Timoteo 1:6 Chifukwa chake ndikukumbutsa iwe ukoleze mphatso ya Mulungu ili mwa iwe mwa kuika kwa manja anga.
IP:Country:City:Region:
|