MAZIKO OKHAZIKIKA 2 - CHIKHULUPILIRO CHA KWA MULUNGU
SERMON TOPIC: MAZIKO OKHAZIKIKA- 2 - CHIKHULUPILIRO CHA KWA MULUNGU
Speaker: David Makiyi
Language: CHICHEWA
Date:
Topic Groups: 1ST PRINCIPLES
Sermon synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Ahebri 11:1-6 Koma chikhulupiriro ndicho chikhazikitso chazinthu zoyembekezeka, chiyesero chazinthu zosapenyeka. Pakuti momwemo anachitidwa umboni. Ndichikhulupiriro Abeli anapereka kwa Mulungu nsembe yoposa ija ya Kaini, imene anachitidwa umboni nayo kuti anali olungama; nachitapo umboni Mulungu pamitulo yake; ndipo momwemo iye angakhale anafa alankhulabe. Ndichikhulupiriro Enoke anatengedwa kuti angaone imfa; ndipo sanapezeka, popeza Mulungu adamtenga: Pakuti asadamtenge anachitidwa umboni kuti anakondweretsa Mulungu; koma wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo ndikuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna iye.
IP:Country:City:Region:
|