Sermon synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Buku la aHebri 5:11-6:3 ma vesi amenewa amafotokoza momveka bwino kuyambira chiyambi mpaka mapeto amoyo wa chi khristu. Akhristu ambiri sakula mmoyo wa uzimu sadziwa zoyambirira za chiphunzitso cha chikhristu. Chiphunzitso cha “Kufunikira kwa Maziko Okhazikika” ndichiphunzitso choyamba mwa ziphunzitso zisanu ndi ziwiri, chimene chimathandizira okhulupirira kumvetsetsa ziphumzitso zina zotsatira kukula mmoyo wa uzimu.