UNGAKHALE BWANJI NKHRISTU OPULUMUTSIDWA
SERMON TOPIC: UNGAKHALE BWANJI NKHRISTU OPULUMUTSIDWA
Speaker: Gavin Paynter
Language: CHICHEWA
Date: 20 April 2013
Topic Groups:
Sermon synopsis: (Mlembi: Gavin Paynter)
(Womasulira: David Makiyi)
Funso lofunikira kwambiri lomwe aliyense angafunse kufunsa lingafanane ndi limene wa ndende wa ku afilipi anafunsa Paulo ndi Sila,”Ambuye ndichitenji kuti ndi pulumuke?”
(Machitidwe 16:30). Ndingakhale bwanji Nkristu wopulumutsidwa kuchilango cha uchimo?Tchimo ndi chiani?
IP:Country:City:Region:
|