Your browser does not support JavaScript

Sermons in CHICHEWA

The Covid-19 Christian
Sermon by Ken Paynter on 24 January 2022
Synopsis: AKHRISTU AMENEWA AMATSATIRA NDONDOMEKO ZA Covid -19 - Amavala maski. - Amakhala motalikirana - Amasamba mmanja. - Amakhala mmanyumba mwawo. - Analandira katemera.
KUUKA KWA AKUFA KWA YESU - 3
Sermon by Gavin Paynter on 4 March 2019
Synopsis: Kuuka kwa kufa kwa Ambuye Yesu ndi chikhulupiliro chakuti Yesu atafa adakhalanso ndi moyo patsiku loyamba lasabata patatha masiku atatu iye ataikidwa mmanda. Mmawu achikhulupiriro chathu muli mawu.....
TCHIMO NDI CHISOMO (Sin and Grace)
Sermon by Ken Paynter on 28 November 2017
Synopsis: Sitiyenera kufuna funa kumene tingakapeze uchimo, uchimo uli kale mkati mwathu. “Zikadakhala zosavuta uchimo ukudakhala mwa anthu owerengeka chifukwa oipawo akadapatulidwa padera ndi.....
TSIKU-LA-ADAMBO
Sermon by Gavin Paynter on 13 July 2017
Synopsis: 1 Yohane 2:13 Ndikulemberani atate popeza mwamzindikira Iye, amene ali kuyambira pachiyambi. Ndikulemberani anyamata popeza mwamulaka oyipayo, ndikulemberani ana popeza mwazindikira Atate......
Calvinism - Part 6a -The atonement - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 26 May 2017
Synopsis: TANTHAUZO ; Mau akuti atonement ndi mau amene alibe mau ambiri owatanthawuzira muchingerezi. Mau akuti atonement adalumikidzidwa ndi ndi William Tyndale ndipo muchingerezi amatanthawuza.....
What is wrong with Christians (CHICHEWA)
Sermon by Ken Paynter on 1 September 2015
Synopsis: KUTEMBENUKA KOSAKHALA KWENIKWENI Kutembenuka mtima ndiko kubadwanso mwatsopano . Panyengo yakutembenuka mtima okhulupirira amasandulika mtima mwa Mzimu Oyera ndipo amayamba ulemdo osiyana ndi.....
KUKHALA NDI MOYO OYAMIKIRA KUSIYANA NDI KUZIKUNDIKIRA
Sermon by Ken Paynter on 23 June 2015
Synopsis: KUZIKUNDIKIRA: Ndi moyo ofuna kukhala ndi zinthu zonse za pamwamba kapena kufuna ulemu wina wapadera. 2 Timoteo 3:1-5 Masiku otsiriza anthu adzakhala osayamika. Chikhalidwe china cha anthu.....
The value of a soul - Part 3 (CHICHEWA)
Sermon by Gavin Paynter on 30 March 2015
Synopsis: Q: Kodi moyo wanu ndi wa mtengo wapatali bwanji kwa inu? A: Moyo wanu ndiye chuma choposa chuma chirichonse chimene mungathe kukhala nacho. Moyo uposa thupi: Mateyu 10:28 Ndipo musamaopa.....
The book of life
Sermon by Gavin Paynter on 15 February 2015
Synopsis: Mneneri wa Mulungu Mose adanena kuti Mulungu ali Ndi Buku la kulembamo: Eksodo 32:32 “… Ngati mukana mundifafanizetu, kundichotsatu mbuku lanu limene munalembera.” Mtumwi Yohane ali kunenana kuti.....
Last words of Jesus - The great commission - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 15 August 2014
Synopsis: Pamene wina ali pafupi kusiyana nafe munjira ya imfa kapenanso ulendo wautali, mau omwe amawalankhula amakhala ofunika kwambiri mwinanso kuposera ena onse omwe adawalankhula kale asanasiyane nanu......
Gossip and the tongue - CHICHEWA
Sermon by Ken Paynter on 1 June 2014
Synopsis: Yakobo 3:9-10 imayamika Ambuye ndi Atate nalo; naloso timatemberera anthu okhala monga mwamafanizidwe a Mulungu. Mochokera mkamwa momwqemo mutuluka chiyamiko ndi temberero. Abale anga izi.....
Chikondi (Love)
Sermon by Ken Paynter on 26 May 2014
Synopsis: Imodzi mwa mitu yamphamvu ya ulakatuli mu Baibulo, 1 Akolinto 13, mtumwiPaulo akufotokoza za mtundu wachikondichomwe akhristuayenera kukhala nacho: “Chikondi chikhala chilezere,chiri chokoma.....
Contentment - CHICHEWA
Sermon by Ken Paynter on 30 April 2014
Synopsis: Ahebri 13:5 “Sindidzakusiyani konse, kungakhale kukutaya, sindidzakutaya ndithu.” Ahebri 13:5 Ndi ndime yodziwika, koma ndi gawo limodzi lavesi, sivesi la thunthu loyima palokha. Ndime yonse ya.....
Matthew 5 - The beatitudes - Part 2 (CHICHEWA)
Sermon by Gavin Paynter on 29 April 2014
Synopsis: Mateyu 5:7 “Odala ali akuchitira chifundo; chifukwa adzalandira chifundo. 8 Odala ali oyera mtima, chifukwa adzaona Mulungu. 9 Odala ali akuchita mtendere; chifukwa adzatchedwa ana a Mulungu. 10.....
Matthew 5 - The beatitudes - Part 1 (CHICHEWA)
Sermon by Gavin Paynter on 26 April 2014
Synopsis: Chiphunzitso cha paphiri ndi m’ndandanda wa ziphunzitso zomwe Yesu adaphunzitsa pa phiri, kuchokera pa Mateyu 5:3-12. Mau akuti Chiphunzitso chapaphiri, mukumasulira kwina kwa chingerezi amatchedwa.....
3 signs - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 17 April 2014
Synopsis: Mateyu analemba zizindikiro zodabwitsa zitatu zimene zinachitika tsiku limene Ambuye Yesu adapachikidwa. 1) Mdima pa dziko lonse la pansi. 2) Chinsalu chotchinga mkachisi chinang’ambika. 3).....
The cares of this life - CHICHEWA
Sermon by Ken Paynter on 5 April 2014
Synopsis: KODI MWAPSINJIKA NDINKHAWA ZA MOYO UNO? MULUNGU AKUTI MUMUTULIRE IYE. 1 PETRO 5:6-7 Potero dzichepetseni pansi pa dzanja la mphamvu la Mulungu, kuti pantawi yache akukwezeni;ndi kutaya pa iye.....
Do Muslims worship the same God as Christians - Part 1 - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 7 March 2014
Synopsis: Pongoyang’ana ndi maso, Chisilamu chiri ndi mayambidwe ofanana ndi zipembedzo za Judaism komanso Chikhristu Asilamu amakhulupilira Mulungu mmodzi , mlengi wa zonse. Chisilamu chidachokera mufuko.....
UTUMIKI WA MZIMU WOYERA
Sermon by Gavin Paynter on 1 March 2014
Synopsis: Q: Kodi cholinga cha ubatizo wa Mzimu Woyera ndi chiyani? Kodi ndi chakuti anthu alankhule ndi malilime ndi kuchita zodabwitsa. Kapena adzigwetse ndimavina vina? A: AYI – Ambuye Yesu adapereka.....
KUFUNA FUNA MZINDA
Sermon by Gavin Paynter on 1 February 2014
Synopsis: Munjira imeneyi, Abrahamu amafaniziridwa ndi a Khristu ammene ali monga alendo padziko lino lapansi, amene mwa chikhulupiliro ali kuyang’anira dziko labwino- dziko lakumwamba. Ahebri 11:13-14 Iwo.....
INU NDINU MCHERE
Sermon by Gavin Paynter on 19 November 2013
Synopsis: MATEYU 5:13-16 “Inu ndinu m’chere wadziko lapansi; koma mcherewo ngati ukasukuluka, adzaukoleretsa ndi chiyani? Pamenepo sungakwanirenso kanthu konse, koma kuti ukaponyedwe kunja nupondedwe ndi.....
ANTHU AKUGWIRA NTCHITO
Sermon by Gavin Paynter on 17 November 2013
Synopsis: 2 Atesalonika 3:6 Ndipo tikulamulirani abale, m’dzina la Ambuye wathu, kuti mubwevuke kwa m’bale yense wakuyenda dwache dwache, osatsata mwambo umene anaulandila kwa ife. Pakuti mudziwa nokha m’mene.....
CHIPHUNZITSO CHA CHIPULUMUTSO - Gawo 2
Sermon by Gavin Paynter on 16 November 2013
Synopsis: Chikhristu chimaphunzitsa kuti Yesu simunthu wamba, mneneri, koma, Mpulumutsi wadziko lonse ,”dzina lokhalo pansi pa thambo lopatsidwa kwa anthu lomwe tipulumutsidwa nalo.” (Machitidwe.....
Chipambano kapena Kukhulupirika (Success or faithfulness)
Sermon by Ken Paynter on 10 November 2013
Synopsis: Mulungu sakutifunsa kuti tikapambane pachiri chonse chimene tirikuchita, koma kuti tikhale okhulupilika. Adatero mayi wina wodziwika ndi ntchito zachifundo wotchedwa. (Mayi Teresa) Nthawi zonse.....
Temptation
Sermon by Gavin Paynter on 10 October 2013
Synopsis: Yesero ndi zochitika zimene zimaoneka zokopa kwa munthu.Makopedwewa amabweretsa kumva kutsutsika chifukwa amatsogolera munthu kukachita chinthu chotsutsana ndi chimene iye amafuna. Mayesero.....
Nkhawa, Kupsinjika mumtima ndi Madandaulo
Sermon by Gavin Paynter on 10 October 2013
Synopsis: Mlakatuli komanso mtumiki wachikhristu ku Scotland, George MacDonald adati; “Sizosamalira moyo zalero, zomwe zimamusautsa munthu, koma zamawa.” “Nkhawa siyikuba chisoni cha mawa, koma imangoyamwa.....
CHOLINGA CHA MASAUTSO
Sermon by Gavin Paynter on 21 September 2013
Synopsis: Baibulo limatipatsa chidwi chochuruka pazimene lima nena za choonadi cheni cheni cha masautso. Ilo sirinena za masautso monga chionongeko monga mnene zipembezo zina zonama zimakhulupirira kapena.....
Mulungu angathe kugwiritsa ntchito aliyense
Sermon by Gavin Paynter on 29 August 2013
Synopsis: Ogulitsa nsapato wina oyambirira wotcedwa D.L. Moody adati “Ngati dziko lapansi lingafikiridwe, Ndiri kutsikimizira kuti, izi ziyenera kuchitika ndi abambo kapena amayi aluso lawo lochuruka. Koma.....
Setting the captives free - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 22 August 2013
Synopsis: KAMASULIRIDWE KA MAWU A UKAPOLO KOLINGANA NDI BAIBULO :Munthu amakhala kapolo wa chilichonse chomwe chimamulamulira: 2 Pet 2:19 ndikuwalonjeza iwo ufulu, pokhala iwo okha ali akapolo a.....
Doctrine of salvation - Part 1 - CHICHEWA
Sermon by Gavin Paynter on 17 July 2013
Synopsis: Chikhristu chimati palibe ngakhale m’modzi angapulumutsidwe kudzera mu ntchito za iye yekha mu umunthu (kupanga miyambo, ntchito zabwino, kudzipatulira kuzinthu zina kapena kulingalira mozama)......
Generational curses (CHICHEWA)
Sermon by Ken Paynter on 6 July 2013
Synopsis: Chinthu ichi chotchedwa themberero chiri ndi maonekedwe amakopedwe kwa anthu ambiri. Nthawi zambiri anthu amene atembenuka mtima magulu aanthu akuda khungu amene anali kupembeza mizimu ya makolo awo.....
KODI MWAKONZEKERA KOKAKHALA MUYAYA
Sermon by Gavin Paynter on 22 June 2013
Synopsis: Anthu ambiri amapanga madongosolo ambiri m’moyo komasadziwa tsiku la imfa yawo. Yakobo 4:13-14 Nanga tsono, inu akunena, lero kapena mmawa tidzapita kulowa kumudzi wakuti wakuti,.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 1b - KUTEMBENUKA KUCHOKA KU NTCHITO ZA KUFA
Sermon by David Makiyi on 8 June 2013
Synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Ahebri 6:1 "... Maziko akutembenuka mtima kusiyana nazo ntchito za kufa ndi chikhulupiriron cha pa Mulungu"
MAZIKO OKHAZIKIKA- 1a - KUFUNIKIRA KWA MAZIKO OKHAZIKIKA
Sermon by David Makiyi on 8 June 2013
Synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Buku la aHebri 5:11-6:3 ma vesi amenewa amafotokoza momveka bwino kuyambira chiyambi mpaka mapeto amoyo wa chi khristu. Akhristu ambiri sakula mmoyo.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 3 - CHIPHUNZITSO CHA UBATIZO
Sermon by David Makiyi on 7 June 2013
Synopsis: Nthawi zambiri timakhala ndi chidziwitso cha ma ubatizo atatu akulu amuBaibulo. Koma tiyenera kudziwa kuti Baibulo limanenanso za ubatizo wa chinayi sikuyenera kukhala osaudziwa. Mu chiphunzitso.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 4 - KUSANJIKA MANJA
Sermon by David Makiyi on 6 June 2013
Synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Mawu otsogolera Mariko 16:17-18 "Ndipo zizindikilo izi zidzawatsata iwo akukhulupilira: mdzina langa adzatulutsa ziwanda; adzalankhula ndi.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 6 - CHIWERUZO CHA MUYAYA
Sermon by David Makiyi on 5 June 2013
Synopsis: Aroma 2:5-11 Koma kolingana ndikuuma kwako,ndimtima wako osalapa, ulikudziunjikira wekha mkwiyo padzuwa la mkwiyo ndi la kubvumbulutsa kuweruza, adzabwezera munthu aliyense kolingana ndi ntchito.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 5 - ZA KUUKA KWA AKUFA
Sermon by David Makiyi on 5 June 2013
Synopsis: Yohane 5:21,24 "Pakuti monga Atate aukitsa akufa, nawapatsa moyo,momwemonso mwana apatsa moyo iwo amene Iye afuna. 24 "Indetu indetu ndinena kwa inu,kuti iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira Iye.....
UNGAKHALE BWANJI NKHRISTU OPULUMUTSIDWA
Sermon by Gavin Paynter on 20 April 2013
Synopsis: (Mlembi: Gavin Paynter) (Womasulira: David Makiyi) Funso lofunikira kwambiri lomwe aliyense angafunse kufunsa lingafanane ndi limene wa ndende wa ku afilipi anafunsa Paulo ndi Sila,”Ambuye.....
MAZIKO OKHAZIKIKA- 2 - CHIKHULUPILIRO CHA KWA MULUNGU
Sermon by David Makiyi on
Synopsis: (Mlembi: Steve Maritz) (Womasulira: David Makiyi) Ahebri 11:1-6 Koma chikhulupiriro ndicho chikhazikitso chazinthu zoyembekezeka, chiyesero chazinthu zosapenyeka. Pakuti momwemo anachitidwa umboni......